Machitidwe 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho mumzindawo munali chimwemwe chachikulu.+ Afilipi 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nthawi zonse kondwerani mwa Ambuye.+ Ndibwerezanso, Kondwerani.+ 1 Petulo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale kuti simunamuonepo, mumamukonda.+ Ngakhale simukumuona panopa, mumakhulupirira mwa iye ndipo mukusangalala kwambiri ndi chimwemwe chachikulu ndiponso chosaneneka,
8 Ngakhale kuti simunamuonepo, mumamukonda.+ Ngakhale simukumuona panopa, mumakhulupirira mwa iye ndipo mukusangalala kwambiri ndi chimwemwe chachikulu ndiponso chosaneneka,