Salimo 64:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wolungama adzakondwera mwa Yehova ndipo adzathawira kwa iye,+Ndipo onse owongoka mtima adzatamanda Mulungu.+ Salimo 104:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kulingalira za iye kukhale kosangalatsa.+Ine ndidzakondwera mwa Yehova.+
10 Wolungama adzakondwera mwa Yehova ndipo adzathawira kwa iye,+Ndipo onse owongoka mtima adzatamanda Mulungu.+