Salimo 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu olungama, kondwerani chifukwa cha zimene Yehova wachita ndipo sangalalani.+Fuulani ndi chisangalalo inu nonse owongoka mtima.+ Salimo 58:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wolungama adzasangalala chifukwa chakuti waona oipa akupatsidwa chilango.+Adzasambitsa mapazi ake m’magazi a anthu oipa.+ Salimo 68:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma olungama asangalale,+Asekerere pamaso pa Mulungu,+Ndipo akondwere ndi kusangalala.+ Afilipi 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nthawi zonse kondwerani mwa Ambuye.+ Ndibwerezanso, Kondwerani.+
11 Inu olungama, kondwerani chifukwa cha zimene Yehova wachita ndipo sangalalani.+Fuulani ndi chisangalalo inu nonse owongoka mtima.+
10 Wolungama adzasangalala chifukwa chakuti waona oipa akupatsidwa chilango.+Adzasambitsa mapazi ake m’magazi a anthu oipa.+