Salimo 52:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Olungama adzaona zimenezi ndi kuchita mantha,+Ndipo adzamuseka.+ Salimo 64:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wolungama adzakondwera mwa Yehova ndipo adzathawira kwa iye,+Ndipo onse owongoka mtima adzatamanda Mulungu.+ Salimo 107:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Olungama amaona ndi kukondwera.+Koma anthu onse osalungama amatseka pakamwa.+ Ezekieli 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu amenewa ndidzawalanga kwambiri ndi kuwadzudzula mwaukali,+ ndipo ndikadzawalanga adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”+ Chivumbulutso 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Kondwerani kumwambako+ chifukwa cha zimene zamuchitikira. Inunso oyera,+ inu atumwi,+ ndi inu aneneri, kondwerani chifukwa Mulungu wamuweruza ndi kumupatsa chilango chifukwa cha zomwe anakuchitirani.”+
10 Wolungama adzakondwera mwa Yehova ndipo adzathawira kwa iye,+Ndipo onse owongoka mtima adzatamanda Mulungu.+
17 Anthu amenewa ndidzawalanga kwambiri ndi kuwadzudzula mwaukali,+ ndipo ndikadzawalanga adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”+
20 “Kondwerani kumwambako+ chifukwa cha zimene zamuchitikira. Inunso oyera,+ inu atumwi,+ ndi inu aneneri, kondwerani chifukwa Mulungu wamuweruza ndi kumupatsa chilango chifukwa cha zomwe anakuchitirani.”+