Ekisodo 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma galu sadzauwa aliyense wa ana a Isiraeli, sadzauwa munthu kapena chiweto,+ kuti mudziwe kuti Yehova akhoza kuchitira ana a Isiraeli zinthu zosiyana ndi zimene angachitire Aiguputo.’+ Salimo 63:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo mfumu idzakondwera mwa Mulungu.+Aliyense wolumbira m’dzina la Mulungu adzam’tamanda,+Pakuti pakamwa pa anthu olankhula chinyengo padzatsekedwa.+ Aroma 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tikudziwa kuti zinthu zonse zimene Chilamulo+ chimanena chimazinena kwa amene ali m’Chilamulo, kuti pakamwa paliponse patsekedwe+ ndipo dziko lonse likhale loyenera+ kulandira chilango cha Mulungu.+
7 Koma galu sadzauwa aliyense wa ana a Isiraeli, sadzauwa munthu kapena chiweto,+ kuti mudziwe kuti Yehova akhoza kuchitira ana a Isiraeli zinthu zosiyana ndi zimene angachitire Aiguputo.’+
11 Ndipo mfumu idzakondwera mwa Mulungu.+Aliyense wolumbira m’dzina la Mulungu adzam’tamanda,+Pakuti pakamwa pa anthu olankhula chinyengo padzatsekedwa.+
19 Tikudziwa kuti zinthu zonse zimene Chilamulo+ chimanena chimazinena kwa amene ali m’Chilamulo, kuti pakamwa paliponse patsekedwe+ ndipo dziko lonse likhale loyenera+ kulandira chilango cha Mulungu.+