Aroma 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Paja Chilamulo chisanabwere, uchimo unalimo kale m’dziko, koma munthu saimbidwa mlandu wa kuchimwa pamene palibe lamulo.+
13 Paja Chilamulo chisanabwere, uchimo unalimo kale m’dziko, koma munthu saimbidwa mlandu wa kuchimwa pamene palibe lamulo.+