Aroma 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kwenikweni, Chilamulo chimabala mkwiyo,+ koma pamene palibe lamulo, palibenso kulakwa.+