Yobu 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Olungama adzaona chiwonongeko chawo n’kusangalala,+Ndipo wosalakwa adzawaseka kuti: Salimo 52:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Olungama adzaona zimenezi ndi kuchita mantha,+Ndipo adzamuseka.+ Salimo 58:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wolungama adzasangalala chifukwa chakuti waona oipa akupatsidwa chilango.+Adzasambitsa mapazi ake m’magazi a anthu oipa.+
19 Olungama adzaona chiwonongeko chawo n’kusangalala,+Ndipo wosalakwa adzawaseka kuti: Salimo 52:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Olungama adzaona zimenezi ndi kuchita mantha,+Ndipo adzamuseka.+ Salimo 58:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wolungama adzasangalala chifukwa chakuti waona oipa akupatsidwa chilango.+Adzasambitsa mapazi ake m’magazi a anthu oipa.+
10 Wolungama adzasangalala chifukwa chakuti waona oipa akupatsidwa chilango.+Adzasambitsa mapazi ake m’magazi a anthu oipa.+