Salimo 68:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kuti musambitse mapazi anu m’magazi,+Kuti malilime a agalu anu anyambite magazi a adani anu.”+ Miyambo 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu woipa ndiye dipo la wolungama,+ ndipo munthu wochita zachinyengo amalowa m’malo mwa anthu owongoka mtima.+ Chivumbulutso 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndipo anapondaponda mopondera mphesamo kunja kwa mzinda,+ ndipo magazi anatuluka m’choponderamo mphesacho mpaka kufika m’zibwano za mahatchi,+ n’kuyenderera mtunda wa masitadiya 1,600.*+
18 Munthu woipa ndiye dipo la wolungama,+ ndipo munthu wochita zachinyengo amalowa m’malo mwa anthu owongoka mtima.+
20 Ndipo anapondaponda mopondera mphesamo kunja kwa mzinda,+ ndipo magazi anatuluka m’choponderamo mphesacho mpaka kufika m’zibwano za mahatchi,+ n’kuyenderera mtunda wa masitadiya 1,600.*+