1 Mafumu 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ukamuuze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Kodi wapha munthu+ n’kutenganso munda wake?”’+ Ukamuuzenso kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Pamalo+ amene agalu ananyambita magazi a Naboti, pomweponso agalu adzanyambita magazi ako, a iweyo.”’”+ 1 Mafumu 22:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Kenako anayamba kutsuka galeta lankhondolo padziwe la ku Samariya ndipo agalu anayamba kunyambita magazi a mfumuyo,+ mogwirizana ndi mawu amene Yehova ananena.+ (Mahule ankasambanso padziwe limeneli.) 2 Mafumu 9:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndiyeno Yehu anati: “M’ponyeni+ pansi Yezebeliyo!” Iwo anam’ponyadi pansi, ndipo magazi ake ena anamwazika n’kuwaza khoma ndi mahatchi. Kenako Yehu anam’pondaponda+ ndi mahatchi ake.
19 Ukamuuze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Kodi wapha munthu+ n’kutenganso munda wake?”’+ Ukamuuzenso kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Pamalo+ amene agalu ananyambita magazi a Naboti, pomweponso agalu adzanyambita magazi ako, a iweyo.”’”+
38 Kenako anayamba kutsuka galeta lankhondolo padziwe la ku Samariya ndipo agalu anayamba kunyambita magazi a mfumuyo,+ mogwirizana ndi mawu amene Yehova ananena.+ (Mahule ankasambanso padziwe limeneli.)
33 Ndiyeno Yehu anati: “M’ponyeni+ pansi Yezebeliyo!” Iwo anam’ponyadi pansi, ndipo magazi ake ena anamwazika n’kuwaza khoma ndi mahatchi. Kenako Yehu anam’pondaponda+ ndi mahatchi ake.