Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 22:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Kenako anayamba kutsuka galeta lankhondolo padziwe la ku Samariya ndipo agalu anayamba kunyambita magazi a mfumuyo,+ mogwirizana ndi mawu amene Yehova ananena.+ (Mahule ankasambanso padziwe limeneli.)

  • 2 Mafumu 9:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Kenako Yehu anauza msilikali wake womuthandiza pagaleta+ dzina lake Bidikara, kuti: “Munyamule, umuponye m’munda wa Naboti Myezereeli.+ Kumbukira kuti iwe ndi ine tinkayenda pambuyo pa Ahabu bambo ake, aliyense atakwera pagaleta lake la mahatchi awiri, pa nthawi imene Yehova anam’temberera+ kuti:

  • Mateyu 7:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 pakuti chiweruzo chimene mukuweruza nacho ena inunso mudzaweruzidwa nacho.+ Ndipo muyezo umene mukuyezera ena, iwonso adzakuyezerani womwewo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena