Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+

      Pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo lidzaterereka poyenda,+

      Pakuti tsiku la tsoka lawo layandikira,+

      Ndipo zowagwera zikufika mofulumira.’+

  • Salimo 119:89
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  89 Inu Yehova, mawu anu anakhazikika kumwamba,+

      Mpaka kalekale.+

  • Yesaya 14:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Pakuti Yehova wa makamu wagamula,+ ndani angazilepheretse?+ Dzanja lake n’limene latambasuka, ndani angalibweze?+

  • Yesaya 46:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ine ndi amene ndimanena za mapeto kuyambira pa chiyambi.+ Kuyambira kalekale, ndimanena za zinthu zimene sizinachitike.+ Ine ndiye amene ndimanena kuti, ‘Zolingalira zanga zidzachitikadi,+ ndipo ndidzachita chilichonse chimene ndikufuna.’+

  • Yesaya 48:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Ndanena zinthu zoyambirira kuchokera pa nthawi imeneyo. Zinatuluka pakamwa panga, ndipo ndinazichititsa kumveka.+ Mwadzidzidzi, ndinazichita ndipo zinachitikadi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena