Salimo 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu a mitundu ina agwera m’dzenje limene anakumba okha.+Phazi lawo lakodwa mu ukonde+ umene anatchera okha.+ Salimo 73:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndithudi, mwawaimika pamalo oterera.+Mwawagwetsa kuti awonongeke.+ Yesaya 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu ambiri pakati pawo adzapunthwa n’kugwa ndi kuthyoka, ndipo adzakodwa n’kugwidwa.+
15 Anthu a mitundu ina agwera m’dzenje limene anakumba okha.+Phazi lawo lakodwa mu ukonde+ umene anatchera okha.+