Mateyu 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wodala amene sapeza chokhumudwitsa mwa ine.”+ Mateyu 21:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Komanso munthu wogwera pamwala umenewu adzaphwanyika. Ndipo aliyense amene mwalawo udzamugwere, udzamupereratu.”+ 1 Akorinto 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 koma ife timalalikira za Khristu amene anapachikidwa.+ Kwa Ayuda, chimenechi ndi chinthu chokhumudwitsa+ ndipo kwa mitundu ina ndi kupusa.+
44 Komanso munthu wogwera pamwala umenewu adzaphwanyika. Ndipo aliyense amene mwalawo udzamugwere, udzamupereratu.”+
23 koma ife timalalikira za Khristu amene anapachikidwa.+ Kwa Ayuda, chimenechi ndi chinthu chokhumudwitsa+ ndipo kwa mitundu ina ndi kupusa.+