Deuteronomo 32:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+Pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo lidzaterereka poyenda,+Pakuti tsiku la tsoka lawo layandikira,+Ndipo zowagwera zikufika mofulumira.’+ Salimo 35:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Awonongeke pamene iwo sakuyembekezera,+Akodwe mu ukonde umene atchera okha.+Agweremo ndi kuwonongeka.+ Miyambo 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Woipa adzagwidwa ndi zolakwa zake zomwe,+ ndipo adzamangidwa m’zingwe za tchimo lake lomwe.+
35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+Pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo lidzaterereka poyenda,+Pakuti tsiku la tsoka lawo layandikira,+Ndipo zowagwera zikufika mofulumira.’+
8 Awonongeke pamene iwo sakuyembekezera,+Akodwe mu ukonde umene atchera okha.+Agweremo ndi kuwonongeka.+