Esitere 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho anapachika Hamani pamtengo+ umene anakonzera Moredekai,+ ndipo mkwiyo wa mfumu unatha. Salimo 69:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tebulo lawo likhale msampha,+Ndipo akodwe ndi chilichonse chimene akusangalala nacho.+ Aroma 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiponso Davide anati: “Tebulo lawo likhale msampha, mbuna, chopunthwitsa ndi chilango kwa iwo.+