Salimo 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye wafukula dzenje, walikumbadi.+Koma adzagwera m’dzenje lokumba yekha.+ Salimo 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu a mitundu ina agwera m’dzenje limene anakumba okha.+Phazi lawo lakodwa mu ukonde+ umene anatchera okha.+ Salimo 57:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwo anditchera ukonde panjira yanga.+Moyo wanga wagwidwa ndi chisoni.+Andikumbira mbuna.Koma iwo agweramo.+ [Seʹlah.] Salimo 141:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Oipa onse adzagwera m’maukonde awo omwe,+Koma ine ndidzadutsa bwinobwino.
15 Anthu a mitundu ina agwera m’dzenje limene anakumba okha.+Phazi lawo lakodwa mu ukonde+ umene anatchera okha.+
6 Iwo anditchera ukonde panjira yanga.+Moyo wanga wagwidwa ndi chisoni.+Andikumbira mbuna.Koma iwo agweramo.+ [Seʹlah.]