Salimo 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Njira yawo ikhale ya mdima ndi yoterera,+Ndipo mngelo wa Yehova aziwathamangitsa. Salimo 37:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pakuti anthu oipa adzatheratu onse,+Ndipo adani a Yehova adzafanana ndi busa la msipu wobiriwira mochititsa kaso.Iwo adzatha.+ Adzazimiririka ndi kusanduka utsi.+ Yeremiya 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Choncho, njira zawo zidzawakhalira ngati malo oterera+ amdima ndipo adzawakankhira m’njirazo moti adzagwa.”+ “Pakuti ndidzawagwetsera tsoka, tsiku la chilango chawo lidzafika,”+ watero Yehova.
20 Pakuti anthu oipa adzatheratu onse,+Ndipo adani a Yehova adzafanana ndi busa la msipu wobiriwira mochititsa kaso.Iwo adzatha.+ Adzazimiririka ndi kusanduka utsi.+
12 “Choncho, njira zawo zidzawakhalira ngati malo oterera+ amdima ndipo adzawakankhira m’njirazo moti adzagwa.”+ “Pakuti ndidzawagwetsera tsoka, tsiku la chilango chawo lidzafika,”+ watero Yehova.