Deuteronomo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+ Yesaya 41:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Tionetseni ndipo mutiuze zinthu zimene zidzachitike. Tiuzeni kuti zinthu zoyambirira zinali zotani, kuti tiziganizire mozama mumtima mwathu ndi kudziwa tsogolo lake. Kapena mutiuze zinthu zimene zikubwera.+ Yesaya 42:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Zinthu zoyamba zachitika,+ koma ndikukuuzani zinthu zatsopano. Zisanayambe kuonekera, ndimakuuzani.”+
15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+
22 “Tionetseni ndipo mutiuze zinthu zimene zidzachitike. Tiuzeni kuti zinthu zoyambirira zinali zotani, kuti tiziganizire mozama mumtima mwathu ndi kudziwa tsogolo lake. Kapena mutiuze zinthu zimene zikubwera.+
9 “Zinthu zoyamba zachitika,+ koma ndikukuuzani zinthu zatsopano. Zisanayambe kuonekera, ndimakuuzani.”+