Genesis 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ine ndidzatulutsa mtundu waukulu mwa iwe. Ndidzakudalitsa ndi kukuza dzina lako, ndipo iwe ukhale dalitso+ kwa ena. Genesis 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma mtundu umene adzautumikirewo ndidzauweruza.+ Pambuyo pake, iwo adzachokako ndi katundu wochuluka.+ Yoswa 21:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Palibe lonjezo ngakhale limodzi limene silinakwaniritsidwe, pa malonjezo onse abwino amene Yehova analonjeza nyumba ya Isiraeli. Onse anakwaniritsidwa.+ 1 Mafumu 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mfumuyo inapitiriza kuti: “Adalitsike Yehova+ Mulungu wa Isiraeli, amene analankhula ndi pakamwa pake kwa Davide+ bambo anga, ndipo ndi dzanja lake wakwaniritsa zimene ananena,+ zakuti,
2 Ine ndidzatulutsa mtundu waukulu mwa iwe. Ndidzakudalitsa ndi kukuza dzina lako, ndipo iwe ukhale dalitso+ kwa ena.
14 Koma mtundu umene adzautumikirewo ndidzauweruza.+ Pambuyo pake, iwo adzachokako ndi katundu wochuluka.+
45 Palibe lonjezo ngakhale limodzi limene silinakwaniritsidwe, pa malonjezo onse abwino amene Yehova analonjeza nyumba ya Isiraeli. Onse anakwaniritsidwa.+
15 Mfumuyo inapitiriza kuti: “Adalitsike Yehova+ Mulungu wa Isiraeli, amene analankhula ndi pakamwa pake kwa Davide+ bambo anga, ndipo ndi dzanja lake wakwaniritsa zimene ananena,+ zakuti,