Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 23:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Tsopano taonani! Ine ndatsala pang’ono kufa.+ Inu mukudziwa bwino ndi mtima wanu wonse ndi moyo wanu wonse, kuti pamawu onse abwino amene Yehova Mulungu wanu ananena kwa inu, palibe ngakhale amodzi omwe sanakwaniritsidwe. Onse akwaniritsidwa kwa inu. Palibe ngakhale mawu amodzi omwe sanakwaniritsidwe.+

  • 1 Samueli 15:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Kuwonjezera apo, Wolemekezeka wa Isiraeli+ sadzalephera kukwaniritsa mawu ake,+ ndipo sadzadzimva kuti ali ndi mlandu, pakuti Iye si munthu kuti adzimve wamlandu.”+

  • 1 Mafumu 8:56
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 56 “Adalitsike Yehova+ amene wapatsa anthu ake Aisiraeli malo ampumulo, monga mwa zonse zimene analonjeza.+ Palibe mawu ndi amodzi omwe+ amene sanakwaniritsidwe pa malonjezo ake onse abwino amene analonjeza kudzera mwa Mose mtumiki wake.+

  • Aheberi 6:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Anachita zimenezo kuti mwa zinthu ziwiri zosasinthika, zimene chifukwa cha zinthu zimenezo n’zosatheka kuti Mulungu aname,+ ife amene tathawira kumalo otetezeka tilimbikitsidwe kwambiri, kuti tigwire mwamphamvu chiyembekezo+ chimene chaikidwa patsogolo pathu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena