Aroma 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chipiriro chimachititsa kuti tikhale ovomerezeka kwa Mulungu.+ Kukhala ovomerezeka kwa Mulungu kumabala chiyembekezo,+ Akolose 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 chimene muli nacho chifukwa cha chiyembekezo+ chodzalandira zimene akusungirani kumwamba.+ Munamva za chiyembekezo chimenechi pamene choonadi cha uthenga wabwino chinalengezedwa kwa inu.+
4 Chipiriro chimachititsa kuti tikhale ovomerezeka kwa Mulungu.+ Kukhala ovomerezeka kwa Mulungu kumabala chiyembekezo,+
5 chimene muli nacho chifukwa cha chiyembekezo+ chodzalandira zimene akusungirani kumwamba.+ Munamva za chiyembekezo chimenechi pamene choonadi cha uthenga wabwino chinalengezedwa kwa inu.+