Aroma 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chotero munthu amakhala ndi chikhulupiriro chifukwa cha zimene wamva.+ Ndipo zimene wamvazo zimachokera m’mawu onena za Khristu.+ Aefeso 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma inunso munakhala ndi chiyembekezo mwa iye mutamva mawu a choonadi,+ omwe ndi uthenga wabwino wonena za chipulumutso chanu.+ Kudzeranso mwa iye, mutakhulupirira munaikidwa chidindo+ cha mzimu woyera wolonjezedwawo,+
17 Chotero munthu amakhala ndi chikhulupiriro chifukwa cha zimene wamva.+ Ndipo zimene wamvazo zimachokera m’mawu onena za Khristu.+
13 Koma inunso munakhala ndi chiyembekezo mwa iye mutamva mawu a choonadi,+ omwe ndi uthenga wabwino wonena za chipulumutso chanu.+ Kudzeranso mwa iye, mutakhulupirira munaikidwa chidindo+ cha mzimu woyera wolonjezedwawo,+