Yohane 4:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Iwo anayamba kuuza mayi uja kuti: “Sikuti tikukhulupirira chifukwa cha mawu ako ajanso ayi, pakuti tadzimvera tokha+ ndipo tadziwa ndithu kuti munthu uyu ndi mpulumutsi+ wa dziko.” Yohane 17:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Sindikupemphera awa okha, komanso amene amakhulupirira ine kudzera m’mawu awo,+
42 Iwo anayamba kuuza mayi uja kuti: “Sikuti tikukhulupirira chifukwa cha mawu ako ajanso ayi, pakuti tadzimvera tokha+ ndipo tadziwa ndithu kuti munthu uyu ndi mpulumutsi+ wa dziko.”