Numeri 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mulungu si munthu, woti anganene mabodza,+Si mwana wa munthu, woti angadzimve kuti ali ndi mlandu.+Kodi ananenapo kanthu koma osachita,Analankhulapo kanthu kodi koma osakwaniritsa?+ Salimo 110:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova walumbira+ (ndipo sadzasintha maganizo). Iye wati:+“Iwe ndiwe wansembe mpaka kalekale,+Monga mwa unsembe wa Melekizedeki!”+ Ezekieli 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsoka lako lidzabwera ndithu+ ndipo ndidzachitapo kanthu. Sindidzazengereza,+ kumva chisoni+ kapena kusintha maganizo.+ Iwo adzakuweruza mogwirizana ndi njira zako ndi zochita zako.+ Ine Yehova ndanena,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
19 Mulungu si munthu, woti anganene mabodza,+Si mwana wa munthu, woti angadzimve kuti ali ndi mlandu.+Kodi ananenapo kanthu koma osachita,Analankhulapo kanthu kodi koma osakwaniritsa?+
4 Yehova walumbira+ (ndipo sadzasintha maganizo). Iye wati:+“Iwe ndiwe wansembe mpaka kalekale,+Monga mwa unsembe wa Melekizedeki!”+
14 Tsoka lako lidzabwera ndithu+ ndipo ndidzachitapo kanthu. Sindidzazengereza,+ kumva chisoni+ kapena kusintha maganizo.+ Iwo adzakuweruza mogwirizana ndi njira zako ndi zochita zako.+ Ine Yehova ndanena,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”