43 “‘Popeza sunakumbukire masiku a ubwana wako+ ndipo unandikwiyitsa ndi zinthu zonsezi,+ ineyo ndidzakubwezera malinga ndi zochita zako.+ Sudzachitanso khalidwe lako lotayirira komanso zinthu zako zonse zonyansa,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.