Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 89:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Ndalumbira kamodzi kokha pa kuyera kwanga,+

      Davide sindidzamunamiza.+

  • Tito 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 kumene kwazikidwa pa chiyembekezo cha moyo wosatha,+ chomwe Mulungu amene sanganame,+ analonjeza kalekale.+

  • Aheberi 6:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Anachita zimenezo kuti mwa zinthu ziwiri zosasinthika, zimene chifukwa cha zinthu zimenezo n’zosatheka kuti Mulungu aname,+ ife amene tathawira kumalo otetezeka tilimbikitsidwe kwambiri, kuti tigwire mwamphamvu chiyembekezo+ chimene chaikidwa patsogolo pathu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena