Salimo 110:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova walumbira+ (ndipo sadzasintha maganizo). Iye wati:+“Iwe ndiwe wansembe mpaka kalekale,+Monga mwa unsembe wa Melekizedeki!”+ Amosi 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, walumbira mwa kuyera kwake+ kuti, ‘“Taonani! Masiku adzafika pamene mudzanyamulidwa ndi ngowe zokolera nyama ndipo otsala anu adzawakola ndi mbedza za nsomba.+ Aheberi 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mofanana ndi zimenezi, Mulungu pofuna kuwatsimikizira kwambiri anthu olandira lonjezolo monga cholowa chawo,+ kuti chifuniro chake n’chosasinthika,+ anachita kulumbira pa zimene analonjezazo.
4 Yehova walumbira+ (ndipo sadzasintha maganizo). Iye wati:+“Iwe ndiwe wansembe mpaka kalekale,+Monga mwa unsembe wa Melekizedeki!”+
2 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, walumbira mwa kuyera kwake+ kuti, ‘“Taonani! Masiku adzafika pamene mudzanyamulidwa ndi ngowe zokolera nyama ndipo otsala anu adzawakola ndi mbedza za nsomba.+
17 Mofanana ndi zimenezi, Mulungu pofuna kuwatsimikizira kwambiri anthu olandira lonjezolo monga cholowa chawo,+ kuti chifuniro chake n’chosasinthika,+ anachita kulumbira pa zimene analonjezazo.