1 Mafumu 8:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 “Atamandike Yehova amene wapatsa anthu ake Aisiraeli malo oti azikhalamo mwamtendere, mogwirizana ndi zimene analonjeza.+ Palibe mawu amene sanakwaniritsidwe pa malonjezo ake onse abwino amene iye analonjeza kudzera mwa Mose mtumiki wake.+
56 “Atamandike Yehova amene wapatsa anthu ake Aisiraeli malo oti azikhalamo mwamtendere, mogwirizana ndi zimene analonjeza.+ Palibe mawu amene sanakwaniritsidwe pa malonjezo ake onse abwino amene iye analonjeza kudzera mwa Mose mtumiki wake.+