Ekisodo 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komabe Farao sadzakumverani,+ motero ndidzaonetsa mphamvu ya dzanja langa pa Iguputo ndi kutulutsa makamu anga,+ anthu anga,+ ana a Isiraeli,+ m’dziko la Iguputo ndi ziweruzo zamphamvu.+ Numeri 33:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa nthawiyi n’kuti Aiguputo ali pa ntchito yoika m’manda ana onse oyamba kubadwa,+ amene Yehova anawapha pakati pawo. Yehovayo anali atapereka ziweruzo pamilungu yawo.+
4 Komabe Farao sadzakumverani,+ motero ndidzaonetsa mphamvu ya dzanja langa pa Iguputo ndi kutulutsa makamu anga,+ anthu anga,+ ana a Isiraeli,+ m’dziko la Iguputo ndi ziweruzo zamphamvu.+
4 Pa nthawiyi n’kuti Aiguputo ali pa ntchito yoika m’manda ana onse oyamba kubadwa,+ amene Yehova anawapha pakati pawo. Yehovayo anali atapereka ziweruzo pamilungu yawo.+