Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 42:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Zinthu zoyamba zachitika,+ koma ndikukuuzani zinthu zatsopano. Zisanayambe kuonekera, ndimakuuzani.”+

  • Yesaya 46:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ine ndi amene ndimanena za mapeto kuyambira pa chiyambi.+ Kuyambira kalekale, ndimanena za zinthu zimene sizinachitike.+ Ine ndiye amene ndimanena kuti, ‘Zolingalira zanga zidzachitikadi,+ ndipo ndidzachita chilichonse chimene ndikufuna.’+

  • Yesaya 48:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 ine ndinakuuzani zonse kuyambira nthawi imeneyo. Ndinakuuzani zisanachitike,+ kuti musadzanene kuti, ‘Fano langa ndi limene lachita zimenezi, ndipo chifaniziro changa chosema komanso chifaniziro changa chopangidwa ndi chitsulo chosungunula, n’zimene zalamula zimenezi.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena