Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 41:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Nenani zinthu zimene zikubwera m’tsogolo, kuti tidziwe kuti inu ndinu milungu.+ Inde, muyenera kuchita zabwino kapena zoipa, kuti tizionere limodzi ndi kuchita mantha.+

  • Yesaya 43:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Taonani! Ndikupanga zinthu zatsopano.+ Zimenezi zionekera ndipo anthu inu muzidziwa ndithu.+ M’chipululu, ine ndidzatsegulamo njira+ ndi mitsinje.+

  • Amosi 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonse asanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+

  • 2 Petulo 1:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Chifukwa ulosi sunayambe wanenedwapo mwa kufuna kwa munthu,+ koma anthu analankhula mawu ochokera kwa Mulungu+ motsogoleredwa ndi mzimu woyera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena