Yesaya 40:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ulemerero wa Yehova ndithu udzaonekera+ ndipo anthu onse adzauonera limodzi,+ pakuti pakamwa pa Yehova m’pamene panena zimenezi.”+ Luka 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu onse adzaona njira ya Mulungu yopulumutsira.’”+
5 Ulemerero wa Yehova ndithu udzaonekera+ ndipo anthu onse adzauonera limodzi,+ pakuti pakamwa pa Yehova m’pamene panena zimenezi.”+