Miyambo 21:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Palibe nzeru kapena kuzindikira kulikonse, kapena malangizo alionse otsutsana ndi Yehova.+ Yesaya 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova wa makamu ndi amene wapereka chigamulo chimenechi,+ kuti anyansitse kukongola kwa mzindawo ndi kuchotsa kunyada kwake,+ ndiponso kuti anyoze anthu onse olemekezeka a padziko lapansi.+ Yesaya 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Inu Yehova, ndinu Mulungu wanga.+ Ndikukukwezani+ ndi kutamanda dzina lanu+ chifukwa mwachita zinthu zabwino kwambiri.+ Mwakwaniritsa zolinga zanu+ zakalekale ndipo mwachita zinthu mokhulupirika+ ndi modalirika.+
9 Yehova wa makamu ndi amene wapereka chigamulo chimenechi,+ kuti anyansitse kukongola kwa mzindawo ndi kuchotsa kunyada kwake,+ ndiponso kuti anyoze anthu onse olemekezeka a padziko lapansi.+
25 Inu Yehova, ndinu Mulungu wanga.+ Ndikukukwezani+ ndi kutamanda dzina lanu+ chifukwa mwachita zinthu zabwino kwambiri.+ Mwakwaniritsa zolinga zanu+ zakalekale ndipo mwachita zinthu mokhulupirika+ ndi modalirika.+