Salimo 33:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zolinga za Yehova zidzakhalapo mpaka kalekale.+Maganizo a mumtima mwake adzakhalapo ku mibadwomibadwo.+ Yesaya 28:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Izi zachokeranso kwa Yehova wa makamu+ amene zolinga zake ndi zabwino kwambiri, ndiponso amene wachita zopambana kwambiri.+ Aheberi 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mofanana ndi zimenezi, Mulungu pofuna kuwatsimikizira kwambiri anthu olandira lonjezolo monga cholowa chawo,+ kuti chifuniro chake n’chosasinthika,+ anachita kulumbira pa zimene analonjezazo.
11 Zolinga za Yehova zidzakhalapo mpaka kalekale.+Maganizo a mumtima mwake adzakhalapo ku mibadwomibadwo.+
29 Izi zachokeranso kwa Yehova wa makamu+ amene zolinga zake ndi zabwino kwambiri, ndiponso amene wachita zopambana kwambiri.+
17 Mofanana ndi zimenezi, Mulungu pofuna kuwatsimikizira kwambiri anthu olandira lonjezolo monga cholowa chawo,+ kuti chifuniro chake n’chosasinthika,+ anachita kulumbira pa zimene analonjezazo.