Salimo 92:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ntchito zanu ndi zazikuludi inu Yehova!+Maganizo anu ndi ozama kwambiri.+ Yesaya 55:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Maganizo a anthu inu si maganizo anga,+ ndipo njira zanga si njira zanu,”+ akutero Yehova. Yeremiya 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Maganizo anga kwa inu ndikuwadziwa bwino. Ndikuganizira+ zokupatsani mtendere osati masoka,+ kuti mukhale ndi chiyembekezo chabwino ndiponso tsogolo labwino,’+ watero Yehova.
11 “‘Maganizo anga kwa inu ndikuwadziwa bwino. Ndikuganizira+ zokupatsani mtendere osati masoka,+ kuti mukhale ndi chiyembekezo chabwino ndiponso tsogolo labwino,’+ watero Yehova.