Yobu 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye ali ndi maganizo amodzi, ndani angam’tsutse?+Zimene moyo wake umalakalaka amazichita.+ Salimo 33:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zolinga za Yehova zidzakhalapo mpaka kalekale.+Maganizo a mumtima mwake adzakhalapo ku mibadwomibadwo.+ Salimo 40:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Yehova Mulungu wanga, mwatichitira zinthu zambiri zodabwitsa,+Ndipo mumatiganizira.+Palibe angafanane ndi inu.+Ndikafuna kulankhula ndi kunena za zodabwitsazo,Zimachuluka kwambiri moti sindingathe kuzifotokoza.+
11 Zolinga za Yehova zidzakhalapo mpaka kalekale.+Maganizo a mumtima mwake adzakhalapo ku mibadwomibadwo.+
5 Inu Yehova Mulungu wanga, mwatichitira zinthu zambiri zodabwitsa,+Ndipo mumatiganizira.+Palibe angafanane ndi inu.+Ndikafuna kulankhula ndi kunena za zodabwitsazo,Zimachuluka kwambiri moti sindingathe kuzifotokoza.+