Salimo 71:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakamwa panga padzanena za chilungamo chanu,+Padzanena za chipulumutso chanu tsiku lonse,+Pakuti ntchito za chilungamo ndi chipulumutso chanu ndi zochuluka ndipo sindinathe kuziwerenga.+ Salimo 139:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nditati ndiyese kuwawerenga, angakhale ochuluka kwambiri kuposa mchenga.+Podzuka ndingakhale ndikuwawerengabe.+
15 Pakamwa panga padzanena za chilungamo chanu,+Padzanena za chipulumutso chanu tsiku lonse,+Pakuti ntchito za chilungamo ndi chipulumutso chanu ndi zochuluka ndipo sindinathe kuziwerenga.+
18 Nditati ndiyese kuwawerenga, angakhale ochuluka kwambiri kuposa mchenga.+Podzuka ndingakhale ndikuwawerengabe.+