Salimo 35:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Lilime langa linene chapansipansi za chilungamo chanu,+Ndipo likutamandeni tsiku lonse.+ Salimo 40:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndanena za uthenga wabwino wachilungamo mumpingo waukulu.+Onani! Sindinatseke pakamwa panga.+Inu Yehova, mukudziwa bwino zimenezi.+
9 Ndanena za uthenga wabwino wachilungamo mumpingo waukulu.+Onani! Sindinatseke pakamwa panga.+Inu Yehova, mukudziwa bwino zimenezi.+