Yesaya 14:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yehova wa makamu walumbira+ kuti: “Ndithu zimene ndaganiza zidzachitika, ndipo zimene ndakonza sizidzalephereka.+ Yesaya 46:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine ndi amene ndimanena za mapeto kuyambira pa chiyambi.+ Kuyambira kalekale, ndimanena za zinthu zimene sizinachitike.+ Ine ndiye amene ndimanena kuti, ‘Zolingalira zanga zidzachitikadi,+ ndipo ndidzachita chilichonse chimene ndikufuna.’+
24 Yehova wa makamu walumbira+ kuti: “Ndithu zimene ndaganiza zidzachitika, ndipo zimene ndakonza sizidzalephereka.+
10 Ine ndi amene ndimanena za mapeto kuyambira pa chiyambi.+ Kuyambira kalekale, ndimanena za zinthu zimene sizinachitike.+ Ine ndiye amene ndimanena kuti, ‘Zolingalira zanga zidzachitikadi,+ ndipo ndidzachita chilichonse chimene ndikufuna.’+