Yesaya 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ndi amene waganiza zochita zimenezi,Kuti athetse kukongola kwa mzindawo komanso kunyada kwake,Kuti achititse manyazi anthu onse amene ankalemekezedwa padziko lonse lapansi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:9 Yesaya 1, ptsa. 249-251
9 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ndi amene waganiza zochita zimenezi,Kuti athetse kukongola kwa mzindawo komanso kunyada kwake,Kuti achititse manyazi anthu onse amene ankalemekezedwa padziko lonse lapansi.+