Yesaya 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova wa makamu ndi amene wapereka chigamulo chimenechi,+ kuti anyansitse kukongola kwa mzindawo ndi kuchotsa kunyada kwake,+ ndiponso kuti anyoze anthu onse olemekezeka a padziko lapansi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:9 Yesaya 1, ptsa. 249-251
9 Yehova wa makamu ndi amene wapereka chigamulo chimenechi,+ kuti anyansitse kukongola kwa mzindawo ndi kuchotsa kunyada kwake,+ ndiponso kuti anyoze anthu onse olemekezeka a padziko lapansi.+