Deuteronomo 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+ Nehemiya 9:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Inu ndinu wolungama+ pa zinthu zonse zimene zatichitikira, pakuti inu mwachita zinthu mokhulupirika+ koma ife tachita zinthu zoipa.+ Salimo 89:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Yehova, kumwamba kudzatamanda ntchito zanu zodabwitsa.+Mpingo wa oyera anu udzatamanda kukhulupirika kwanu.
4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+
33 Inu ndinu wolungama+ pa zinthu zonse zimene zatichitikira, pakuti inu mwachita zinthu mokhulupirika+ koma ife tachita zinthu zoipa.+
5 Inu Yehova, kumwamba kudzatamanda ntchito zanu zodabwitsa.+Mpingo wa oyera anu udzatamanda kukhulupirika kwanu.