Deuteronomo 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo iwe ukudziwa bwino kuti Yehova Mulungu wako ndi Mulungu woona,+ Mulungu wokhulupirika,+ wosunga pangano+ ndiponso wosonyeza kukoma mtima kosatha kwa anthu amene amam’konda ndi kusunga malamulo ake ku mibadwo masauzande,+ 2 Samueli 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Munthu wokhulupirika, mudzamuchitira mokhulupirika.+Munthu wamphamvu wopanda cholakwa, mudzamuchitira mwachilungamo.+
9 Ndipo iwe ukudziwa bwino kuti Yehova Mulungu wako ndi Mulungu woona,+ Mulungu wokhulupirika,+ wosunga pangano+ ndiponso wosonyeza kukoma mtima kosatha kwa anthu amene amam’konda ndi kusunga malamulo ake ku mibadwo masauzande,+
26 Munthu wokhulupirika, mudzamuchitira mokhulupirika.+Munthu wamphamvu wopanda cholakwa, mudzamuchitira mwachilungamo.+