-
Yesaya 49:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Yehova, Wowombola Isiraeli,+ Woyera wake, wauza yemwe ananyozedwa kwambiri,+ yemwe amadedwa ndi mtundu wa anthu,+ mtumiki wa atsogoleri,+ kuti: “Mafumu adzaimirira chifukwa cha zimene adzaone,+ ndipo akalonga adzagwada chifukwa cha Yehova. Iye ndi wokhulupirika,+ Woyera wa Isiraeli, amene anakusankha.”+
-
-
2 Akorinto 1:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Koma Mulungu ndi wodalirika kuti mawu athu kwa inu asakhale Inde kenako Ayi.
-