Salimo 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zakumwamba zikulengeza ulemerero wa Mulungu.+Ndipo m’mlengalenga mukufotokoza ntchito ya manja ake.+ Salimo 50:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo kumwamba kukunena za chilungamo chake,+Pakuti Mulungu ndiye Woweruza.+ [Seʹlah.] Salimo 97:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kumwamba kwalengeza za chilungamo chake,+Ndipo mitundu yonse ya anthu yaona ulemerero wake.+
19 Zakumwamba zikulengeza ulemerero wa Mulungu.+Ndipo m’mlengalenga mukufotokoza ntchito ya manja ake.+