Numeri 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndingathe bwanji kutemberera anthu amene Mulungu sanawatemberere?+Anthu amene Yehova sanawaitanire tsoka, ndingathe bwanji kuwaitanira tsoka?+ Miyambo 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mumtima mwa munthu mumakhala zolinga zambiri,+ koma zolinga za Yehova n’zimene zidzakwaniritsidwe.+ Machitidwe 5:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma ngati ikuchokera kwa Mulungu,+ simungathe kuwaletsa.+ Mukaumirira mukhoza kupezeka kuti mukulimbana ndi Mulungu.”+ Aroma 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+
8 Ndingathe bwanji kutemberera anthu amene Mulungu sanawatemberere?+Anthu amene Yehova sanawaitanire tsoka, ndingathe bwanji kuwaitanira tsoka?+
21 Mumtima mwa munthu mumakhala zolinga zambiri,+ koma zolinga za Yehova n’zimene zidzakwaniritsidwe.+
39 Koma ngati ikuchokera kwa Mulungu,+ simungathe kuwaletsa.+ Mukaumirira mukhoza kupezeka kuti mukulimbana ndi Mulungu.”+
31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+