Yesaya 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Yehova, mudzachita chilungamo kuti mutipatse mtendere,+ pakuti ntchito zathu zonse tazikwanitsa chifukwa cha inu.+ Aroma 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+
12 Inu Yehova, mudzachita chilungamo kuti mutipatse mtendere,+ pakuti ntchito zathu zonse tazikwanitsa chifukwa cha inu.+
31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+