Machitidwe 5:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Choncho mmene zinthu zilili panopa, ndikukuuzani kuti, Alekeni amuna amenewa musalimbane nawo. Chifukwa ngati zolinga zawo kapena ntchito iyi ikuchokera kwa anthu, sipita patali.+ Machitidwe 5:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma ngati ikuchokera kwa Mulungu,+ simungathe kuwaletsa.+ Mukaumirira mukhoza kupezeka kuti mukulimbana ndi Mulungu.”+
38 Choncho mmene zinthu zilili panopa, ndikukuuzani kuti, Alekeni amuna amenewa musalimbane nawo. Chifukwa ngati zolinga zawo kapena ntchito iyi ikuchokera kwa anthu, sipita patali.+
39 Koma ngati ikuchokera kwa Mulungu,+ simungathe kuwaletsa.+ Mukaumirira mukhoza kupezeka kuti mukulimbana ndi Mulungu.”+