Machitidwe 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno tonse titagwa pansi, ndinamva mawu akundiuza m’Chiheberi kuti, ‘Saulo, Saulo, n’chifukwa chiyani ukundizunza ine? Ukungovutika popitiriza kuchita ngati nyama imene ikuponya miyendo yake kuti imenye zisonga zotosera.’*+
14 Ndiyeno tonse titagwa pansi, ndinamva mawu akundiuza m’Chiheberi kuti, ‘Saulo, Saulo, n’chifukwa chiyani ukundizunza ine? Ukungovutika popitiriza kuchita ngati nyama imene ikuponya miyendo yake kuti imenye zisonga zotosera.’*+